1 Samueli 9:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo panali munthu Mbenjamini, dzina lake ndiye Kisi, mwana wa Abiyele, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya, mwana wa Mbenjamini, ndiye ngwazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo panali munthu Mbenjamini, dzina lake ndiye Kisi, mwana wa Abiyele, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya, mwana wa Mbenjamini, ndiye ngwazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Panali munthu wina wotchuka, wa ku dera la Benjamini, dzina lake Kisi, mwana wa Abiyele, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya, wa fuko la Benjamini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Panali munthu wina wa fuko la Benjamini, wotchuka, dzina lake Kisi, mwana wa Abieli, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya. Onani mutuwo |