1 Samueli 8:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Yehova anati kwa Samuele, Umvere mau ao, nuwalongere mfumu. Ndipo Samuele anati kwa amuna a Israele, Mupite, munthu yense kumzinda wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Yehova anati kwa Samuele, Umvere mau ao, nuwalongere mfumu. Ndipo Samuele anati kwa amuna a Israele, Mupite, munthu yense kumudzi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Tsono Chauta adauza Samuele kuti, “Umvere zimene akunena, ndipo uŵapatse mfumu.” Choncho Samuele adauza Aisraelewo kuti, “Nonse bwererani kwanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Yehova anamuyankha nati, “Amvere zimene akunena ndipo apatse mfumu.” Ndipo Samueli anati kwa Aisraeli aja, “Bwererani aliyense kwawo.” Onani mutuwo |