Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 8:21 - Buku Lopatulika

21 Ndipo Samuele anamva mau onse a anthuwo, nawafotokozanso m'makutu a Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo Samuele anamva mau onse a anthuwo, nawafotokozanso m'makutu a Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Samuele atamva mau onse a anthuwo, adakakambira Chauta mau onsewo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Samueli atamva zonse zimene anthuwo ananena, iye anakazifotokozanso kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 8:21
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Hezekiya analandira kalatayo ku dzanja la mithenga, namwerenga, nakwera Hezekiya kunka kunyumba ya Yehova, namfunyulula pamaso pa Yehova.


Pamenepo Yefita anamuka ndi akulu a Giliyadi, ndipo anthu anamuika mkulu wao ndi mtsogoleri wao; ndipo Yefita ananena mau ake onse pamaso pa Yehova ku Mizipa.


Ndipo Yehova anati kwa Samuele, Umvere mau ao, nuwalongere mfumu. Ndipo Samuele anati kwa amuna a Israele, Mupite, munthu yense kumzinda wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa