1 Samueli 8:5 - Buku Lopatulika5 nanena naye, Taonani, mwakalamba, ndipo ana anu satsanza makhalidwe anu; tsono, mutilongere mfumu kuti ikatiweruze, monga umo muchitidwa m'mitundu yonse ya anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 nanena naye, Taonani, mwakalamba, ndipo ana anu satsanza makhalidwe anu; tsono, mutilongere mfumu kuti ikatiweruze, monga umo muchitidwa m'mitundu yonse ya anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Adamuuza kuti, “Taonani, inu tsopanotu mwakhwima, ndipo ana anu sali ndi makhalidwe onga anu. Tsono mutipatse mfumu kuti izitilamulira, monga m'mene ikuchitira mitundu ina ya anthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iwo anati kwa iye “Taonani, inu mwakula tsopano ndipo ana anu sakutsata makhalidwe anu abwino. Tsono mutipatse mfumu kuti izitilamulira, monga momwe ikuchitira mitundu ina yonseyi.” Onani mutuwo |