1 Samueli 8:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo idzatenga limodzi la magawo khumi la mbeu zanu, ndi la minda yanu yampesa, nidzalipatsa akapitao ake, ndi anyamata ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo idzatenga limodzi la magawo khumi la mbeu zanu, ndi la minda yanu yamphesa, nidzalipatsa akapitao ake, ndi anyamata ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Idzalanda gawo lachikhumi la tirigu wanu ndi la mphesa zanu, nidzapatsa kwa akapitao ake ndi nduna zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Idzatenga gawo lakhumi la tirigu wanu ndi mphesa zanu ndi kupereka kwa nduna zake ndi akapitawo ake. Onani mutuwo |