1 Samueli 8:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo idzatenga akapolo anu, ndi adzakazi anu, ndi anyamata anu okongola koposa, ndi abulu anu, nidzawagwiritsa ntchito yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo idzatenga akapolo anu, ndi adzakazi anu, ndi anyamata anu okongola koposa, ndi abulu anu, nidzawagwiritsa ntchito yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Idzakulandani antchito anu aamuna ndi adzakazi anu. Idzakulandaninso ng'ombe zanu zonenepa ndi abulu anu, ndi kumazigwiritsa ntchito zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mfumuyo idzatenga antchito anu aamuna ndi aakazi. Idzatenganso ngʼombe zanu zabwino ndi abulu anu nʼkumazingwiritsa ntchito. Onani mutuwo |