1 Samueli 8:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo idzatenga ana anu aakazi apange zonunkhira, naphikire, naumbe mikate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo idzatenga ana anu akazi apange zonunkhira, naphikire, naumbe mikate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Izidzatenga ana anu aakazi kuti azidzayenga mafuta onunkhira, ndi kumaphika chakudya ndi kumapanga buledi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iyo idzatenga ana anu akazi kuti akhale oyenga mafuta onunkhira, ophika chakudya ndi kupanga buledi. Onani mutuwo |