1 Samueli 8:12 - Buku Lopatulika12 idzawaika akhale otsogolera chikwi, ndi otsogolera makumi asanu; ndipo idzaika ena kulima minda yake, ndi kutema dzinthu zake, ndi kumpangira zipangizo za nkhondo, ndi zipangizo za magaleta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 idzawaika akhale otsogolera chikwi, ndi otsogolera makumi asanu; ndipo idzaika ena kulima minda yake, ndi kutema dzinthu zake, ndi kumpangira zipangizo za nkhondo, ndi zipangizo za magaleta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ena idzaŵaika kuti akhale olamulira ankhondo chikwi chimodzi kapena makumi asanu. Ndipo ena azidzalima kumunda kwake ndi kumakolola zolima zake, kusula zida zankhondo ndiponso zipangizo za magaleta ankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ena adzawayika kukhala olamulira asilikali 1,000, ena olamulira asilikali makumi asanu, ndi ena otipula minda yake, ndi kukolola ndiponso ena adzakhala osula zida zankhondo ndi zida za magaleta ake. Onani mutuwo |