1 Samueli 6:6 - Buku Lopatulika6 Mulikuumitsiranji mitima yanu, monga Aejipito ndi Farao anaumitsa mitima yao? Kodi iwo sanalole anthuwo amuke, Iye atachita kodabwitsa pakati pao, ndipo anamuka? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mulikuumitsiranji mitima yanu, monga Aejipito ndi Farao anaumitsa mitima yao? Kodi iwo sanalole anthuwo amuke, Iye atachita kodabwitsa pakati pao, ndipo anamuka? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Chifukwa chiyani mukufuna kukhala okanika ngati Aejipito aja ndi Farao? Kodi Aejipitowo, Mulungu ataŵazunza, suja adaŵalola Aisraele kuti apite, ndipo adapitadi? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nʼchifukwa chiyani mukuwumitsa mitima monga anachita Aigupto ndi Farao? Mulungu atawalanga anthu a ku Igupto aja kodi suja anawalola Aisraeli kuti azipita ndipo anapitadi? Onani mutuwo |