1 Samueli 6:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo pamene mafumu asanu a Afilisti anaonerako, anabwerera kunka ku Ekeroni tsiku lomwelo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo pamene mafumu asanu a Afilisti anaonerako, anabwerera kunka ku Ekeroni tsiku lomwelo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Akalonga asanu a Afilisti aja ataona zimenezo, adabwerera ku Ekeroni tsiku lomwelo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Atsogoleri asanu a Afilisti ataona izi anabwerera ku Ekroni tsiku lomwelo. Onani mutuwo |