1 Samueli 6:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ng'ombezo zinatsata njira yolunjika ku Betesemesi, zinali kuyenda mumseu, zilikulira; sizinapatukire ku dzanja lamanja, kapena kulamanzere; ndipo mafumu a Afilisti anazitsatira kufikira ku malire a Betesemesi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ng'ombezo zinatsata njira yolunjika ku Betesemesi, niziyenda mumseu, zilikulira poyenda; sizinapatukira ku dzanja lamanja, kapena kulamanzere; ndipo mafumu a Afilisti anazitsatira kufikira ku malire a Betesemesi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono ng'ombezo zidapita molunjika potsata mseu waukulu wokafika ku Betesemesi, zikunka zikulira. Sizidacheukire kumanzere kapena kumanja, ndipo akalonga a Afilisti ankazitsata pambuyo, mpaka kukafika ku malire a ku Betesemesi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ngʼombe zija zinapita molunjika kutsata msewu wopita ku Beti Semesi zikulira njira yonse. Sizinakhotere kumanja kapena kumanzere. Akalonga a Afilisti anazitsatira mpaka mʼmalire a Beti-Semesi. Onani mutuwo |