1 Samueli 6:11 - Buku Lopatulika11 naika likasa la Yehova pagaletapo, ndi bokosi m'mene munali mbewa zagolide ndi zifanizo za mafundo ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 naika likasa la Yehova pagaletapo, ndi bokosi m'mene munali mbewa zagolide ndi zifanizo za mafundo ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ndipo adaika Bokosi lachipangano pa galeta, ndi bokosi lija m'mene munali mbeŵa zagolide ndi zifanizo za mafundo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsono anayika Bokosi la Yehova pa galeta pamodzi ndi bokosi limene munali makoswe agolide ndi zifanizo zawo za zithupsa. Onani mutuwo |