1 Samueli 6:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anthuwo anatero; natenga ng'ombe ziwiri zamkaka, nazimanga pagaleta, natsekera anao kwao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anthuwo anatero; natenga ng'ombe ziwiri zamkaka, nazimanga pagaleta, natsekera anao kwao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Anthu aja adachitadi momwemo. Adatenga ng'ombe ziŵiri zamkaka nazimanga ku galeta, natsekera makonyani ake m'khola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Anthu aja anachitadi zimenezi. Anatenga ngʼombe zamkaka ziwiri nazimanga ku galeta lija. Koma ana awo anawatsekera mʼkhola. Onani mutuwo |