1 Samueli 5:5 - Buku Lopatulika5 Chifukwa chake angakhale ansembe, angakhale ena akulowa m'nyumba ya Dagoni, palibe woponda pa chiundo cha Dagoni ku Asidodi, kufikira lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Chifukwa chake angakhale ansembe, angakhale ena akulowa m'nyumba ya Dagoni, palibe woponda pa chiundo cha Dagoni ku Asidodi, kufikira lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chimenechi ndicho chifukwa chake chimene ansembe a Dagoni ndi anthu onse amene amaloŵa m'nyumba ya Dagoni, sapondera pa chiwundo cha nyumbayo ku Asidodi, mpaka pano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Nʼchifukwa chake mpaka lero ansembe a Dagoni kapena wina aliyense amene amalowa mʼkachisi wa Dagoni ku Asidodi saponda pa khonde. Onani mutuwo |