1 Samueli 5:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo amene anapanda kufa anagwidwa ndi mafundowo; ndi kulira kwa mzindawo kunakwera kumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo amene anapanda kufa anagwidwa ndi mafundowo; ndi kulira kwa mudziwo kunakwera kumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Anthu amene sadafe, adavutika ndi mafundo, ndipo kulira kwa anthu amumzindamo kudamveka mpaka kumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Anthu amene sanafe anavutika ndi zithupsa, ndipo kulira kwa anthu a mu mzindamo kunamveka kumwamba. Onani mutuwo |