1 Samueli 6:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo likasa la Yehova linakhala ku dziko la Afilisti miyezi isanu ndi iwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo likasa la Yehova linakhala ku dziko la Afilisti miyezi isanu ndi iwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Bokosi lachipangano la Chauta lidakhala m'dziko la Afilisti miyezi isanu ndi iŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Bokosi la Yehova linakhala mʼdziko la Afilisti kwa miyezi isanu ndi iwiri. Onani mutuwo |