1 Samueli 5:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Afilisti anatenga likasa la Mulungu, nachoka nalo ku Ebenezeri, napita ku Asidodi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Afilisti anatenga likasa la Mulungu, nachoka nalo ku Ebenezeri, napita ku Asidodi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Afilisti atalanda Bokosi lachipangano lija, adalinyamula kuchoka nalo ku Ebenezeri nakafika nalo ku Asidodi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Afilisti atalanda Bokosi la Mulungu lija, analitenga kuchoka ku Ebenezeri kupita ku Asidodi. Onani mutuwo |