1 Samueli 4:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo iye anati, Ulemerero wachoka kwa Israele; chifukwa likasa la Mulungu lalandidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo iye anati, Ulemerero wachoka kwa Israele; chifukwa likasa la Mulungu lalandidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Mau ake anali omwewo akuti, “Ulemerero wachoka kwa Aisraele poti Bokosi lachipangano la Chauta lalandidwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ananena momwemo kuti, “Ulemerero wachoka mu Israeli, pakuti Bokosi la Mulungu lalandidwa.” Onani mutuwo |