1 Samueli 31:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo nkhondoyo inamkulira Saulo kwambiri, oponya mivi nampeza; ndipo iye anasautsika kwakukulu chifukwa cha oponya miviyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo nkhondoyo inamkulira Saulo kwambiri, oponya mivi nampeza; ndipo iye anasautsika kwakukulu chifukwa cha oponya miviyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nkhondo idampanikiza kwambiri Sauloyo, ndipo anthu amauta adampeza namlasa koopsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nkhondo inakula kwambiri mozungulira Sauli ndipo pamene anthu amauta anamupeza, anamuvulaza kwambiri. Onani mutuwo |