1 Samueli 31:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anaika zida zake m'nyumba ya Asitaroti; napachika mtembo wake ku linga la ku Beteseani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anaika zida zake m'nyumba ya Asitaroti; napachika mtembo wake ku linga la ku Beteseani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono adaika zida zankhondo za Sauloyo m'nyumba yopembedzeramo Asitaroti, mulungu wao. Ndipo adakhomerera mtembo wake ku khoma la mzinda wa Betisani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Iwo anayika zida zake zankhondo mʼnyumba yopembedzera Asitoreti, ndipo thupi lake analikhomera pa khoma la mzinda wa Beti-Sani. Onani mutuwo |