1 Samueli 30:2 - Buku Lopatulika2 nagwira akazi ndi onse anali m'mwemo, aakulu ndi aang'ono; sanaphe mmodzi, koma anawatenga, namuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 nagwira akazi ndi onse anali m'mwemo, akulu ndi ang'ono; sanaphe mmodzi, koma anawatenga, namuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adatenga akazi kuti akhale akapolo, pamodzi ndi onse amene anali m'menemo, aang'ono ndi aakulu omwe. Sadaphepo ndi mmodzi yemwe, koma adaŵatenga amoyo napita nawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Anatenga akazi ndi onse amene anali mʼmenemo akuluakulu ndi angʼono omwe kuti akakhale akapolo. Sanaphe aliyense koma anawatenga amoyo napita nawo. Onani mutuwo |