1 Samueli 30:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo sikanasoweka kanthu, kakang'ono kapena kakakulu, ana aamuna kapena ana aakazi, kapena chuma kapena china chilichonse cha zija anazitenga iwowa; Davide anabwera nazo zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo sikanasoweka kanthu, kakang'ono kapena kakakulu, ana amuna kapena ana akazi, kapena chuma kapena china chilichonse cha zija anazitenga iwowa; Davide anabwera nazo zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Panalibe kanthu kalikonse kamene kadasoŵapo. Adalanditsa ana aamuna ndi ana aakazi, ndiponso chilichonse chimene chidaatengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Palibe chimene chinasowa anthu onse, kuyambira wamngʼono mpaka wamkulu, mnyamata mpaka mtsikana anapulumutsidwa. Davide anapulumutsa chilichonse chimene anafunkha Aamaleki aja. Onani mutuwo |