1 Samueli 30:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Davide analanditsa zonse anazitenga Aamaleke, napulumutsa akazi ake awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Davide analanditsa zonse anazitenga Aamaleke, napulumutsa akazi ake awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Motero Davide adalanditsa zinthu zonse zimene adaatenga Aamaleke. Ndipo adapulumutsanso akazi ake aŵiri aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Choncho Davide analanditsa zinthu zonse zimene Aamaleki aja anatenga. Anapulumutsanso akazi ake awiri aja. Onani mutuwo |