1 Samueli 3:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Aisraele onse, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba anazindikira kuti Samuele anakhazikika akhale mneneri wa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Aisraele onse, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba anazindikira kuti Samuele anakhazikika akhale mneneri wa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ndipo Aisraele onse, kuyambira ku Dani mpaka ku Beereseba, adadziŵa kuti Chauta adamsankha Samuele kuti akhale mneneri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ndipo Aisraeli onse kuyambira ku dera la Dani mpaka ku Beeriseba anazindikira kuti Yehova analozadi chala pa Samueli kuti akhale mneneri wake. Onani mutuwo |