1 Samueli 3:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Samuele anakula, Yehova nakhala naye, osalola kuti mau ake amodzi apite pachabe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Samuele anakula, Yehova nakhala naye, osalola kuti mau ake amodzi apite pachabe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Monse Samuele ankakula, Chauta anali naye, motero zonse zimene Samueleyo ankanena zinkachitikadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Yehova anali ndi Samueli pamene amakula, ndipo zonse zimene ankayankhula zinkachitikadi. Onani mutuwo |