1 Samueli 3:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Samuele anamuuza zonse, sanambisire kanthu. Ndipo iye anati, Ndiye Yehova; achite chomkomera pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Samuele anamuuza zonse, sanambisire kanthu. Ndipo iye anati, Ndiye Yehova; achite chomkomera pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Choncho Samuele adamuuza zonse osambisira kanthu kalikonse. Ndipo Eli adati, “Ameneyo ndi Chauta. Nachite zimene zikumkomera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Choncho Samueli anamuwuza zonse, sanamubisire kalikonse. Ndipo Eli anati, “Iye ndi Yehova, mulekeni achite chimene chamukomera.” Onani mutuwo |