1 Samueli 3:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Yehova anaonekanso mu Silo, pakuti Yehova anadziwulula kwa Samuele ku Silo, mwa mau a Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Yehova anaonekanso m'Silo, pakuti Yehova anadziwulula kwa Samuele ku Silo, mwa mau a Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Chauta ankadziwululabe ku Silo. Kumeneko ankamveketsa mau ake kwa Samuele polankhula naye. Ndipo mau ake a Samuele ankafika kwa Aisraele onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Yehova anapitiriza kuoneka ku Silo, ndipo kumeneko anadziwulula yekha kwa Samueli mwa mawu ake. Onani mutuwo |