Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 29:5 - Buku Lopatulika

5 Uyu si Davide kodi amene anamthirirana mang'ombe m'magulu ao, kuti, Saulo anapha zikwi zake, koma Davide zikwi zake zankhani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Uyu si Davide kodi amene anamthirirana mang'ombe m'magulu ao, kuti, Saulo anapha zikwi zake, koma Davide zikwi zake zankhani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ameneyutu ndi Davide, yemwe uja ankamuvinira ndi kumuimbira kuti, “ ‘Saulo wapha zikwi inde, koma Davide wapha zikwi khumikhumi?’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Paja ameneyu ndi Davide yemwe ankamuvinira namuyimbira kuti, “ ‘Sauli wapha anthu 1,000 koma Davide wapha miyandamiyanda?’ ”

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 29:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Miriyamu mneneriyo, mlongo wa Aroni, anagwira lingaka m'dzanja lake; ndipo akazi onse anatuluka kumtsata ndi malingaka ndi kuthira mang'ombe.


Yemwe adalitsa mnzake ndi mau aakulu pouka mamawa, anthu adzachiyesa chimenecho temberero.


Ndipo anyamata a Akisi ananena naye, Uyu si Davide mfumu ya dzikolo kodi? Sanathirirana mang'ombe za iye kodi m'magule ao, ndi kuti, Saulo anapha zikwi zake, koma Davide zikwi zake zankhani?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa