1 Samueli 29:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo akalonga a Afilisti ananyamuka ndi mazana ao ndi zikwi zao; ndipo Davide ndi anthu ake ananyamuka ndi a pambuyo pamodzi ndi Akisi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo akalonga a Afilisti ananyamuka ndi mazana ao ndi zikwi zao; ndipo Davide ndi anthu ake ananyamuka ndi a pambuyo pamodzi ndi Akisi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pamene atsogoleri ankhondo a Afilisti ankatsogoza magulu ao a ankhondo mazana angapo ndiponso zikwi zingapo, Davide ndi ankhondo ake ankayenda pambuyo ndi Akisi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pamene atsogoleri a Afilisti ankatsogolera magulu awo ankhondo a miyandamiyanda, Davide ndi ankhondo ake ankayenda pambuyo pamodzi ndi Akisi. Onani mutuwo |