1 Samueli 28:25 - Buku Lopatulika25 nabwera nazo kwa Saulo ndi kwa anyamata ake; nadya iwowa. Atatero ananyamuka, nachoka usiku womwewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 nabwera nazo kwa Saulo ndi kwa anyamata ake; nadya iwowa. Atatero ananyamuka, nachoka usiku womwewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono adadzapereka bulediyo kwa Saulo ndi nduna zake, ndipo onse adadya. Pambuyo pake adanyamuka, nachokapo usiku womwewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Tsono anapereka bulediyo kwa Sauli ndi nduna zake ndipo anadya. Pambuyo pake ananyamuka kupita kwawo usiku womwewo. Onani mutuwo |