Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 28:24 - Buku Lopatulika

24 Ndipo mkaziyo anali ndi mwanawang'ombe wonenepa m'nyumbamo; ndipo anafulumira, namupha, natenga ufa naukanyanga mkate wopanda chotupitsa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Ndipo mkaziyo anali ndi mwanawang'ombe wonenepa m'nyumbamo; ndipo anafulumira, namupha, natenga ufa naukanyanga mkate wopanda chotupitsa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Mkaziyo anali ndi mwanawang'ombe wonenepa, ndipo adamupha mwachangu. Adatenga ufa naukanyanga, naphika buledi wosatupitsidwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Mkaziyo anali ndi mwana wangʼombe wonenepa ndipo anamupha mwachangu. Anatenga ufa nawukanyanga ndipo anaphika buledi wopanda yisiti.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 28:24
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Abrahamu analowa msanga m'hema wake kwa Sara, nati, Konza msanga miyeso itatu ya ufa wosalala, nuumbe, nupange mikate.


ndipo idzani naye mwanawang'ombe wonenepa, mumuphe, ndipo tidye, tisekere;


Ndipo uyu anati kwa iye, Mng'ono wako wafika; ndipo atate wako anapha mwanawang'ombe wonenepa, chifukwa anamlandira iye wamoyo.


nabwera nazo kwa Saulo ndi kwa anyamata ake; nadya iwowa. Atatero ananyamuka, nachoka usiku womwewo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa