Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 27:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo Akisi anampatsa Zikilagi tsiku lomweli; chifukwa chake Zikilagi ndi wa mafumu a Yuda kufikira lero lomwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo Akisi anampatsa Zikilagi tsiku lomweli; chifukwa chake Zikilagi ndi wa mafumu a Yuda kufikira lero lomwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Choncho tsiku limenelo Akisi adapatsa Davide mudzi wa Zikilagi. Nchifukwa chake mudzi wa Zikilagi ngwa mafumu a Yuda mpaka lero lino.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Choncho tsiku limenelo Akisi anamupatsa Zikilagi ndipo mzindawo wakhala wa mafumu a Yuda mpaka lero.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 27:6
12 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali atamwalira Saulo, pamene Davide anabwera atawapha Aamaleke, ndipo Davide atakhala ku Zikilagi masiku awiri;


Anadzawo kwa Davide ku Zikilagi, akali chitsekedwere chifukwa cha Saulo mwana wa Kisi, ndi awa; ndiwo mwa amphamvuwo omthandiza kunkhondo.


Pomuka iye ku Zikilagi anapatukira kwa iye a Manase: Adina, ndi Yozabadi, ndi Yediyaele, ndi Mikaele, ndi Yozabadi, ndi Elihu, ndi Ziletai, akulu a zikwi a ku Manase.


ndi ku Betuele, ndi ku Horoma, ndi ku Zikilagi,


ndi mu Zikilagi, ndi mu Mekona ndi midzi yake,


ndi Zikilagi, ndi Madimana ndi Sanisana;


ndi Zikilagi, ndi Betemara-Kaboti, ndi Hazara-Susa:


popeza iye anataya moyo wake nakantha Mfilistiyo, ndipo Yehova anachitira Aisraele onse chipulumutso chachikulu, inu munachiona, nimunakondwera; tsono mudzachimwiranji mwazi wosalakwa, ndi kumupha Davide popanda chifukwa?


Ndipo Davide anati kwa Akisi, Ngati mwandikomera mtima, andipatse malo kumudzi kwina kuminda, kuti ndikakhale kumeneko; pakuti mnyamata wanu adzakhala bwanji mu mzinda wachifumu pamodzi ndi inu?


Koma akalonga a Afilisti anapsa naye mtima; nanena naye akalonga a Afilisti, Bwezani munthuyu, abwerere kumalo kwake kumene munamuikako, asatsikire nafe kunkhondo, kuti kunkhondoko angasanduke mdani wathu; pakuti uyu adzadziyanjanitsa ninji ndi mfumu yake? Si ndi mitu ya anthu awa?


Ndipo kunali, pakufika Davide ndi anthu ake ku Zikilagi tsiku lachitatu, Aamaleke adaponya nkhondo yovumbulukira kumwera, ndi ku Zikilagi, nathyola Zikilagi nautentha ndi moto;


Tinathira nkhondo kumwera kwa Akereti ndi ku dziko lija la Ayuda, ndi kumwera kwa Kalebe; ndipo tinatentha mudzi wa Zikilagi ndi moto.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa