1 Samueli 27:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo kuwerenga kwake kwa masiku Davide anakhala ku dziko la Afilisti ndiko chaka chimodzi ndi miyezi inai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo kuwerenga kwake kwa masiku Davide anakhala ku dziko la Afilisti ndiko chaka chimodzi ndi miyezi inai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Motero Davide adakhala ku dziko la Afilisti chaka chimodzi ndi miyezi inai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Davide anakhala mʼdziko la Afilisti kwa chaka chimodzi ndi miyezi inayi. Onani mutuwo |