1 Samueli 25:6 - Buku Lopatulika6 ndipo muzitero kwa wodalayo, Mtendere ukhale pa inu, mtendere ukhalenso pa nyumba yanu, ndi mtendere ukhale pa zonse muli nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 ndipo muzitero kwa wodalayo, Mtendere ukhale pa inu, mtendere ukhalenso pa nyumba yanu, ndi mtendere ukhale pa zonse muli nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mukamulonjere motere: mukati mbuye wathu akuti, ‘Mtendere ukhale ndi inu ndi banja lanu ndi zinthu zonse zimene muli nazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mukamuwuze kuti, ‘Mtendere ukhale ndi inu, banja lanu pamodzi ndi zonse zimene muli nazo. Onani mutuwo |