Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 25:44 - Buku Lopatulika

44 Pakuti Saulo anapatsa Mikala, mwana wake, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Laisi, wa ku Galimu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

44 Pakuti Saulo anapatsa Mikala, mwana wake, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Laisi, wa ku Galimu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

44 Paja Saulo anali atakwatitsa mwana wake Mikala, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Laisi wa ku Galimu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

44 Koma Sauli anali atakwatitsa Mikala, mkazi wa Davide kwa Paliti mwana wa Laisi wa ku Galimu.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 25:44
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide anatumiza mithenga kwa Isiboseti mwana wa Saulo, nati, Undipatse mkazi wanga Mikala amene ndinadzitomera ndi nsonga za makungu za Afilisti zana limodzi.


Pomwepo Isiboseti anatumiza namchotsera kwa mwamuna wake, kwa Palatiele mwana wa Laisi.


Fuula ndi mau ako iwe mwana wamkazi wa Galimu! Tamva, iwe Laisa! Iwe Anatoti wosauka!


Ndipo Mikala mwana wamkazi wa Saulo anakonda Davide; ndipo pakumva Saulo, anakondwera nako.


Ndipo asanathe masikuwo, ananyamuka Davide, ndi anthu ake, nakaphako Afilisti mazana awiri, ndipo Davide anatenga nsonga za makungu ao nazipatsa mofikira kwa mfumu, kuti akhale mkamwini wa mfumu. Ndipo Saulo anampatsa Mikala mwana wake wamkazi akhale mkazi wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa