1 Samueli 26:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Azifi anafika kwa Saulo ku Gibea, nati, Kodi Davide sali kubisala m'phiri la Hakila, kupenya kuchipululu! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Azifi anafika kwa Saulo ku Gibea, nati, Kodi Davide sali kubisala m'phiri la Hakila, kupenya kuchipululu! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina anthu a ku Zifi adabwera kwa Saulo ku Gibea, namuuza kuti, “Davide akubisala ku phiri la Hakila limene lili kuvuma kwa Yesimoni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Anthu a ku Zifi anapita kwa Sauli ku Gibeya nati, “Davide akubisala ku phiri la Hakila, limene limayangʼanana ndi Yesimoni.” Onani mutuwo |