1 Samueli 25:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo kudatero pakuberekeka iye pabulu wake, natsikira pamalo obisika a m'phirilo, onani, Davide ndi anthu ake analikutsikira kwa iye; iye nakomana nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo kudatero pakuberekeka iye pa bulu wake, natsikira pa malo obisika a m'phirilo, onani, Davide ndi anthu ake analikutsikira kwa iye; iye nakomana nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono mkaziyo atakwera pa bulu ndi kufika patsinde pa phiri lina, adangoona Davide ndi ankhondo ake akubwera kwa iye. Ndipo mkaziyo adakumana nawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Mayi uja atakwera pa bulu wake ndi kufika pa tsinde la phiri, anangoona Davide ndi ankhondo ake akubwera kunali iye. Choncho anakumana nawo. Onani mutuwo |