Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 25:19 - Buku Lopatulika

19 Nati kwa anyamata ake, Nditsogolereni; onani ndidza m'mbuyo mwanu. Koma sanauze mwamuna wake Nabala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Nati kwa anyamata ake, Nditsogolereni; onani ndidza m'mbuyo mwanu. Koma sanauze mwamuna wake Nabala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Kenaka adauza anyamata ake antchito kuti, “Batsogolani, ine ndikudza pambuyo panu.” Koma sadauze Nabala mwamuna wake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Kenaka anawuza antchito ake kuti, “Tsogolani, ine ndikutsatirani.” Koma sanawuze mwamuna wake Nabala.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 25:19
9 Mawu Ofanana  

Ndipo anazipereka zimenezo m'manja a anyamata ake, gulu pa lokha gulu pa lokha: ndipo anati kwa anyamata ake, Taolokani patsogolo panga, tachitani danga pakati pa magulu, lina ndi lina.


Ndipo anauzanso wachiwiri ndi wachitatu, ndi onse anatsata magulu, kuti, Muzinena kwa Esau chotero, pamene mukomana naye:


ndiponso muziti, Ndiponso, taonani, kapolo wanu Yakobo ali pambuyo pathu. Pakuti anati, Ndidzampembedzera iye ndi mphatso imene ipita patsogolo panga, pambuyo pake ndidzaona nkhope yake; kapena adzandilandira ine.


Momwemo naolotsa mphatso patsogolo pake: ndipo iye yekha anagona usiku womwewo pachigono.


Ayang'anira mayendedwe a banja lake, sadya zakudya za ulesi.


Ndipo kunali tsiku lina kuti Yonatani mwana wa Saulo ananena ndi mnyamata wonyamula zida zake, Tiye tipite kunka ku kaboma ka Afilisti, tsidya lija. Koma sanauze atate wake.


Ndipo kudatero pakuberekeka iye pabulu wake, natsikira pamalo obisika a m'phirilo, onani, Davide ndi anthu ake analikutsikira kwa iye; iye nakomana nao.


Ndipo Abigaile anafika kwa Nabala; ndipo, onani, anali ndi madyerero m'nyumba mwake, monga madyerero a mfumu; ndi mtima wa Nabala unasekera kwambiri m'kati mwake, pakuti analedzera kwambiri; m'mwemo uyo sadamuuze kanthu konse, kufikira kutacha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa