1 Samueli 25:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo panali munthu ku Maoni, amene katundu wake anali ku Karimele; iyeyu anali womveka ndithu, anali nazo nkhosa zikwi zitatu, ndi mbuzi chikwi chimodzi; ndipo analikusenga nkhosa zake ku Karimele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo panali munthu ku Maoni, amene katundu wake anali ku Karimele; iyeyu anali womveka ndithu, anali nazo nkhosa zikwi zitatu, ndi mbuzi chikwi chimodzi; ndipo analikusenga nkhosa zake ku Karimele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono panali munthu wina ku Maoni amene anali ndi kadziko ku dera la mudzi wa Karimele. Munthuyo anali wolemera kwambiri. Anali ndi nkhosa 3,000 ndi mbuzi 1,000. Tsiku lina adayamba kumeta nkhosa zake ku Karimele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kunali munthu wina wolemera kwambiri ku Maoni amene malo ake a ntchito anali ku Karimeli. Iyeyu anali ndi mbuzi 1,000 ndi nkhosa 3,000. Onani mutuwo |