1 Samueli 24:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo kunali m'tsogolo mwake kuti mtima wa Davide unamtsutsa chifukwa adadula mkawo wa mwinjiro wa Saulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo kunali m'tsogolo mwake kuti mtima wa Davide unamtsutsa chifukwa adadula mkawo wa mwinjiro wa Saulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Koma pambuyo pake Davideyo adavutika mumtima mwake, chifukwa chakuti anali atadula chidutswa chija ku mkanjo wa Saulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Atachita izi, Davide anatsutsika mu mtima chifukwa anadula msonga ya mkanjo wa Sauli. Onani mutuwo |