1 Samueli 24:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Davide analumbirira Saulo. Saulo namuka kwao; koma Davide ndi anthu ake anakwera kunka kungaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Davide analumbirira Saulo. Saulo namuka kwao; koma Davide ndi anthu ake anakwera kunka kungaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Davide adalumbira zonsezi Saulo alikumva. Tsono Saulo adabwerera kwao, koma Davide ndi anthu ake adapitanso kuphanga kobisalira kuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Choncho Davide analumbira pamaso pa Sauli. Pambuyo pake Sauli anabwerera kwawo, koma Davide ndi anthu ake anapitanso ku phanga kuja. Onani mutuwo |