1 Samueli 24:21 - Buku Lopatulika21 Chifukwa chake tsono undilumbirire ndi Yehova, kuti sudzatha mbeu yanga nditamuka ine, ndi kuti sudzaononga dzina langa m'nyumba ya atate wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Chifukwa chake tsono undilumbirire ndi Yehova, kuti sudzatha mbeu yanga nditamuka ine, ndi kuti sudzaononga dzina langa m'nyumba ya atate wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Undilonjeze molumbira tsono m'dzina la Chauta kuti sudzapha zidzukulu zanga ine nditamwalira, kuti dzina langa ndi la abambo anga lisaiŵalike.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Tsopano undilonjeze molumbira lero mʼdzina la Yehova kuti sudzapha zidzukulu zanga ine nditamwalira kapena kufuta dzina langa pa banja la makolo anga.” Onani mutuwo |