1 Samueli 24:17 - Buku Lopatulika17 Nati kwa Davide, Iwe ndiwe wolungama woposa ine; popeza unandibwezera zabwino, koma ine ndinakubwezera zoipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Nati kwa Davide, Iwe ndiwe wolungama woposa ine; popeza unandibwezera zabwino, koma ine ndinakubwezera zoipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Adauza Davide kuti, “Iwe wachita chilungamo kupambana ine, pakuti wandichitira ine zabwino pamene ine ndakuchita zoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Anawuza Davide kuti, “Ndiwe wolungama kuposa ine. Iwe wandikomera mtima pamene ine ndakuchitira zoyipa. Onani mutuwo |