1 Samueli 24:13 - Buku Lopatulika13 Monga umanena mwambi wa makolo, kuti, Uchimo utulukira mwa ochimwa; koma dzanja langa silidzakhala pa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Monga umanena mwambi wa makolo, kuti, Uchimo utulukira mwa ochimwa; koma dzanja langa silidzakhala pa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Paja anthu akale adati, ‘Munthu woipa, ntchito zake nzoipa.’ Motero ine sindikupwetekani, ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Paja anthu akale anati, ‘Munthu woyipa, ntchito zakenso ndi zoyipa.’ Kotero dzanja langa silidzakukhudzani. Onani mutuwo |