1 Samueli 23:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Davide anadziwa kuti Saulo analikulingalira zomchitira zoipa; nati kwa Abiyatara wansembe, Bwera kuno ndi efodi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Davide anadziwa kuti Saulo analikulingalira zomchitira zoipa; nati kwa Abiyatara wansembe, Bwera kuno ndi efodi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma Davide adaadziŵa kuti Saulo akufuna kumchita chiwembu. Choncho adauza wansembe Abiyatara kuti abwere ndi efodi ija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Davide atadziwa kuti Sauli akufuna kumuchita chiwembu, anawuza Abiatara wansembe uja kuti, “Bwera nayo efodiyo.” Onani mutuwo |