1 Samueli 23:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Saulo anamemeza anthu onse kunkhondo, kuti atsikire ku Keila, kumangira misasa Davide ndi anthu ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Saulo anamemeza anthu onse kunkhondo, kuti atsikire ku Keila, kumangira misasa Davide ndi anthu ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Saulo adasonkhanitsa ankhondo ake, naŵatuma ku Keila kuti akamzinge Davide pamodzi ndi anthu ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Choncho Sauli anasonkhanitsa ankhondo ake nawatuma ku Keila kuti akamuzungulire Davide ndi anthu ake. Onani mutuwo |