1 Samueli 23:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anthu anauza Saulo kuti Davide wafika ku Keila. Ndipo Saulo anati, Mulungu wampereka m'dzanja langa; pakuti atsekerezeka, popeza analowa m'mudzi wa zitseko ndi mipiringidzo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anthu anauza Saulo kuti Davide wafika ku Keila. Ndipo Saulo anati, Mulungu wampereka m'dzanja langa; pakuti atsekerezeka, popeza analowa m'mudzi wa zitseko ndi mipiringidzo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Saulo atamva kuti Davide wafika ku Keila, adati, “Mulungu wampereka m'manja mwanga. Pamene waloŵa mu mzinda umene uli ndi zipata ndi mipiringidzo yolimba, ndiye kuti wadzimanga yekha.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Sauli atamva kuti Davide wapita ku Keila anati, “Mulungu wamupereka kwa ine, pakuti Davide wadzitsekera yekha mʼndende polowa mu mzinda umene uli ndi zipata ndi zotsekera zake.” Onani mutuwo |