1 Samueli 23:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Saulo ndi anthu ake anamuka kukamfuna. Koma wina anauza Davide; chifukwa chake anatsikira kuthanthweko, nakhala m'chipululu cha Maoni. Ndipo pamene Saulo anamva ichi, iye anamlondola Davide m'chipululu cha Maoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Saulo ndi anthu ake anamuka kukamfuna. Koma wina anauza Davide; chifukwa chake anatsikira kuthanthweko, nakhala m'chipululu cha Maoni. Ndipo pamene Saulo anamva ichi, iye anamlondola Davide m'chipululu cha Maoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono Saulo ndi anthu ake adapita kukamfunafuna Davide, koma iye anali atazimva. Nchifukwa chake adathaŵa napita ku thanthwe la ku chipululu cha Maoni. Saulo atamva kuti Davide adathaŵira ku Maoni, adamlondola kuchipululu komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Sauli ndi anthu ake anapita kukamufufuza Davide. Koma Davide atamva izi anathawa ndi kukabisala ku thanthwe la chipululu cha Maoni. Sauli atamva kuti Davide anathawira ku Maoni anamutsatira ku chipululu komweko. Onani mutuwo |