1 Samueli 23:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo iwo ananyamuka, namuka ku Zifi asanapiteko Saulo; koma Davide ndi anthu ake anali ku chipululu cha Maoni, m'chigwa cha kumwera kwa chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo iwo ananyamuka, namuka ku Zifi asanapiteko Saulo; koma Davide ndi anthu ake anali ku chipululu cha Maoni, m'chigwa cha kumwera kwa chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Anthuwo adabwerera ku Zifi, Saulo asananyamuke. Pa nthaŵiyo Davide ndi anthu ake anali ku chipululu cha Maoni ku Araba, kumwera kwa Yesimoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Kotero iwo ananyamuka ndi kupita ku Zifi, koma Sauli asananyamuke. Nthawi imeneyi Davide ndi anthu ake anali ku chipululu cha Maoni, ku Araba kummwera kwa Yesimoni. Onani mutuwo |