1 Samueli 23:23 - Buku Lopatulika23 Chifukwa chake yang'anirani, ndi kudziwa ngaka zonse alikubisalamo iye, nimubwere kwa ine ndi mau otsimikizika, pomwepo ndidzamuka nanu; ndipo akakhala m'dzikomo, ndidzampwaira pakati pa mabanja onse a Yuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Chifukwa chake yang'anirani, ndi kudziwa ngaka zonse alikubisalamo iye, nimubwere kwa ine ndi mau otsimikizika, pomwepo ndidzamuka nanu; ndipo akakhala m'dzikomo, ndidzampwaira pakati pa mabanja onse a Yuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Nchifukwa chake muwone malo onse amene amabisalako, ndipo mubwerenso kuno kuti mudzandiwuze chenicheni. Tsono ndidzapita nanu. Ndipo ngati alidi kumeneko, ndidzamfunafuna pakati pa anthu onse m'dziko lonse la Yuda.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kafufuzeni ndithu malo onse kumene amabisalako, ndipo mubwerenso kuno mudzandiwuze chenicheni. Pambuyo pake ine ndidzapita nanu. Ngatidi ali mʼderalo ndidzamusaka pakati pa mabanja onse a Yuda.” Onani mutuwo |